Hoseya
MUTU1
1MauaYehovaameneanadzakwaHoseyamwanawa BeerimasikuaUziya,Yotamu,Ahazi,ndiHezekiya, mafumuaYuda,ndimasikuaYerobiamumwanawa YoasimfumuyaIsrayeli.
2ChiyambichamawuaYehovamwaHoseyaNdipo YehovaanatikwaHoseya,Muka,udzitengeremkazi wacigololondianaacigololo; 3NdipoanamukanatengaGomerimwanawamkaziwa Dibulaimu;ameneanatengapakati,nambaliraiyemwana wamwamuna.
4NdipoYehovaanatikwaiye,Umutchedzinalake Yezreeli;pakutikwatsalakanthawikochepa,ndipo ndidzabwezerachilangomwaziwaYezreelipanyumbaya Yehu,ndikuletsaufumuwanyumbayaIsrayeli
5Ndipokudzachitikatsikulimenelo,kutindidzathyolauta waIsiraelim’chigwachaYezreeli.
6Ndipoanatengansopakati,nabalamwanawamkazi; NdipoYehovaanatikwaiye,Mumutchedzinalake Loruhama;komandidzawacotsakonse.
7KomandidzachitirachifundonyumbayaYuda,+ndipo ndidzawapulumutsa+ndiYehovaMulunguwawo,+ndipo sindidzawapulumutsandiuta,+lupanga,+nkhondo, akavalo+kapenaapakavalo
8NdipopameneanaletsakuyamwaLoruhama,anatenga pakati,nabalamwanawamwamuna.
9PamenepoMulunguanati,Um’tchuledzinalakutiLoami; 10KomakuwerengakwaanaaIsrayelikudzakhalangati mchengawakunyanja,wosayesedwakapena kuwerengedwa;ndipokudzakhala,kutipamalopamene kudanenedwakwaiwo,Simulianthuanga,kumeneko kudzanenedwakwaiwo,InundinuanaaMulungu wamoyo
11PamenepoanaaYudandianaaIsrayeli adzasonkhanitsidwapamodzi,nadzadziikiramtsogoleri mmodzi,nadzatulukam’dziko;pakutitsikulaYezreeli lidzakhalalalikuru
MUTU2
1Nenanikwaabaleanu,Amayi;ndikwaalongoanu, Ruhama
2Kambananindiamayianu,tsutsani:pakutiiyesimkazi wanga,kapenainesindinemwamunawake;
3kutindisamuvulewamaliseche,ndikumuikaiyemonga tsikulijaanabadwa,ndikumuyesaiyengatichipululu,ndi kumuikaiyengatidzikolouma,ndikumuphaiyendiludzu
4Ndiposindidzachitirachifundoanaake;pakutialianaa chigololo.
5Pakutikunyinawacitacigololo,wakuwabalawacita zonyansa;
6Chifukwachake,taona,ndidzatchinganjirayakondi minga,ndidzamangampanda,kutiasapezenjirazake
7Ndipoadzatsataabwenziake,komasadzawapeza;ndipo adzawafunafuna,komasadzawapeza;pamenepoadzati, Ndidzapitandikubwererakwamwamunawangawoyamba; pakutipamenepokunalikwainekoposatsopano
8Pakutisanadziwakutindinampatsatirigu,ndivinyo,ndi mafuta,ndikumcurukitsirasilivandigolide,zimene anakonzeraBaala.
9Cifukwacacendidzatengatiriguwangam’nyengoyace, ndivinyowangam’nyengoyace;
10Tsopanondidzaululachiwerewerechakepamasopa okondedwaake,ndipopalibeameneadzam’landitse m’dzanjalanga
+11Ndidzathetsansochisangalalochakechonse,+ madyereroake,+mweziwokhalamwezi,+masabataake +ndimapwandoakeonseopatulika
+12Ndidzawonongampesawake+ndimitengoyakeya mkuyu+imeneanati,‘Izindimphotozangazimene ondikondaanandipatsa
+13Ndidzam’langa+chifukwachamasikuaAbaala+ ameneanawafukiziransembezofukiza,+ndipo anadzikongoletsandindolo+zakendizokometserazake,+ n’kutsatamabwenziake,+n’kundiiwala,”+watero Yehova
14Chifukwachake,taonani,ndidzamunyengerera,ndi kumtengerakuchipululu,ndikulankhulanayemotonthoza. 15Ndipondidzampatsamindayakeyamphesakuchokera kumeneko,ndichigwachaAkorichikhalekhomola chiyembekezo;
16Ndipopadzakhalatsikulimenelo,atiYehova,kuti udzanditchaIneIsi;ndiposimudzanditchansoBaali 17PakutindidzachotsamayinaaAbaalam’kamwamwake, ndiposadzakumbukiridwansom’dzinalawo
18Ndipotsikulimenelondidzawachitirapanganondi zilombozakuthengo,ndimbalamezam’mlengalenga,ndi zokwawapadzikolapansi:ndipondidzathyolauta,ndi lupanga,ndinkhondopadzikolapansi,ndikuwagonetsa pansimosatekeseka
19Ndipondidzakutomeraukhalewangakosatha;inde, ndidzakutomeraukhalewangam’cilungamo,ndi m’ciweruzo,ndim’cikondi,ndim’cifundo.
20Ndipondidzakutomeraukhalewangamokhulupirika; ndipoudzadziwaYehova.
21Ndipopadzakhalatsikulimenelo,ndidzayankha,ati Yehova,ndidzayankhakumwamba,ndipoiwoadzayankha dzikolapansi;
22Ndipodzikolapansilidzayankhatirigu,ndivinyo,ndi mafuta;ndipoiwoadzamvaYezreeli
23Ndipondidzabzaliraiyepadzikolapansi;ndipo ndidzachitirachifundoiyeamenesanalandirechifundo; ndipondidzatikwaiwoamenesianthuanga,Inundinu anthuanga;ndipoadzati,InundinuMulunguwanga.
MUTU3
1PamenepoYehovaanatikwaine,Pitanso,kondamkazi wokondedwandibwenzilake,komawacigololo,monga mwacikondicaYehovapaanaaIsrayeli,akupenyera milunguyina,nakondamphesazavinyo
2Ndipondinamguliraiyendindalamakhumindizisanu zasiliva,ndihomerilabarele,ndithekalahomerilabarele; 3Ndipondinatikwaiye,Uzikhalakwainemasikuambiri; usachitechigololo,usakhalewamwamunawina; momwemonsondidzakhalakwaiwe.
4PakutianaaIsrayeliadzakhalamasikuambiriopanda mfumu,ndikalonga,opandansembe,opandafano,efodi, ndiaterafi;
+5PambuyopakeanaaIsiraeliadzabwerera+ndi kufunafunaYehovaMulunguwawo+ndiDavidemfumu yawondipoadzaopaYehovandiubwinowakem’masiku otsiriza.
MUTU4
1ImvanimauaYehova,inuanaaIsrayeli;pakutiYehova alindimlandundiokhalam’dziko,popezapalibecoonadi, kapenacifundo,kapenakudziwaMulungum’dzikomo
2Pakulumbira,kunama,ndikupha,ndikuba,ndikuchita chigololo;
3Chifukwachakedzikolidzalira,ndiyensewokhalamo adzalefuka,pamodzindizilombozakuthengo,ndimbalame zam’mlengalenga;inde,nsonsombazam’nyanja zidzachotsedwa.
4Komamunthuasatsutsane,kapenakudzudzulawina; pakutianthuakoalingatiakutsutsanandiwansembe
5Chifukwachakeudzagwausana,mnenerinsoadzagwa pamodzindiiweusiku,ndipondidzawonongaamako
6Anthuangaaonongekachifukwachakusowachidziwitso; popezawakanakudziwa,Inensondidzakukana,kuti usakhalewansembewanga;popezawaiwalachilamulocha Mulunguwako,Inensondidzayiwalaanaako
7Pameneanachuluka,momwemoanandichimwira: chifukwachakendidzasandutsaulemererowawoukhale manyazi
8Iwoamadyazolakwazaanthuanga,ndipomitimayawo amaikam’zolakwazawo
9Ndipopadzakhala,mongaanthu,mongawansembe; ndipondidzawalangachifukwachanjirazawo,ndi kuwabwezerantchitozawo
10Pakutiadzadya,komaosakhuta;adzachitauhule, osachuluka;
11Uhulendivinyondivinyowatsopanozichotsamtima
12Anthuangaafunsirauphungupamitengoyawo,ndipo ndodoyawoimawafotokozera;
13Apheransembepamwambapamapiri,nafukiza zofukizapazitunda,pansipamitengoikuluikulu,ndi mipingo,ndimitsinje,chifukwamthunziwakendi wabwino;
14Sindidzalangaanaanuaakazipameneachitachigololo, kapenaakazianuaakazipochitachigololo;
15Ngakhaleiwe,Israyeli,ucitacigololo,komaYuda asapatuke;ndipomusadzafikekuGiligala,kapenakukwera kuBetaveni,kapenakulumbira,Yehovaalimoyo.
16PakutiIsrayeliwabwereram’mbuyongating’ombe yamphongoyobwereram’mbuyo;
17Efraimuwaphatikanandimafano;
18Chakumwachawochilichowawa;Achitachigololo kosaleka; 19Mphepoyamumangam’mapikoake,ndipoadzachita manyazichifukwachansembezawo
MUTU5
1Imvaniizi,inuansembe;ndipoimvani,inuanyumbaya Israyeli;ndipotcheranikhutu,inuam’nyumbayamfumu; +Pakutichiweruzo+chilikwainu,+chifukwamunali ngatimsamphapaMizipa+ndiukondewoyalidwapa Tabori
2Ndipoopandukawoachulukirakupha,ngakhaleine ndawadzudzulaonsewo.
+3InendikudziwaEfuraimu+ndipoIsiraelisanabisike kwaine,+pakutitsopanoiweEfuraimu,+wachita chigololo+ndipoIsiraeliwadetsedwa.
4ZochitazawosizidzalolakutembenukirakwaMulungu wawo;
5KunyadakwaIsrayelikumchitiraumbonipamasopake; chifukwachakeIsrayelindiEfraimuadzagwam’zolakwa zao;Yudanayensoadzagwapamodzinawo
6Iwoadzapitandinkhosazawonding’ombezawo kukafunafunaYehova;komasadzampeza;wadzipatula kwaiwo.
+7AnachitiraYehovachinyengo+chifukwaanabereka anaachilendo
8LizanilipengakuGibeya,ndilipengakuRama;fuulani kuBetaveni;pambuyopanu,Benjamini
9Efraimuadzakhalabwinjapatsikulachidzudzulo; 10AkalongaaYudaalingatianthuochotsamalire; chifukwachakendidzawatsanuliraukaliwangangatimadzi
11Efraimuwaponderezedwandipowathyoledwa m’chiweruzo,+chifukwaanatsatiramalangizowo mofunitsitsa
12CifukwacacendidzakhalakwaEfraimungatinjenjete, ndikwanyumbayaYudamongacovunda;
13Efraimuataonakudwalakwake,ndiYudaanaonabala lake,EfraimuanapitakwaAsuri,natumizakwamfumu Yarebe;
14PakutikwaEfraimundidzakhalangatimkango,ndi mwanawamkangokwanyumbayaYuda;ndidzamutenga, ndipopalibewomupulumutsa.
15Ndidzamukandikubwererakumaloanga,mpaka avomerezakulakwakwawo,nadzafunankhopeyanga;
MUTU6
1Tiyeni,tibwererekwaYehova;pakutiwang'amba, nadzatichiritsa;watikantha,nadzatimanga
2Atapitamasikuawiriadzatitsitsimutsa:tsikulachitatu adzatiukitsa,ndipotidzakhalandimoyopamasopake.
3Pamenepotidzadziwa,ngatitilondolakumdziwaYehova: kuturukakwakekwakonzekangatim’bandakucha;ndipo adzatidzerangatimvula,mongamvulayamasikandi yophukirapadzikolapansi
4IweEfraimu,ndikuchitirechiyani?IweYuda, ndidzakuchitiraiwechiyani?pakutiubwinowanuulingati mtambowam’mamawa,ndingatimameakumkamamawa
5Chifukwachakendawadulamwaaneneri;Ndinawapha ndimauapakamwapanga;
6Pakutindinafunachifundo,sinsembe;ndikudziwa Mulungukoposansembezopsereza
7Komaiwoalakwirapanganomongaanthu;pamenepo andichitirazachiwembu
8Gileadindimudziwaiwoakuchitamphulupulu, waipitsidwandimwazi
9Ndipomongamaguluaachifwambaamadikiriramunthu, momwemonsogululaansembelimaphaanthum’njira mwakuvomera;
10Ndaonachinthuchonyansam’nyumbayaIsrayeli:pali damalaEfraimu,Israyeliwadetsedwa.
11Ndiponso,iweYuda,wakukonzerazokolola,pamene ndinabwezaundendewaanthuanga
1NdikafunakuciritsaIsrayeli,mphulupuluyaEfraimu idavumbuluka,ndikuipakwaSamariya;ndipombalailowa, ndikhamulaachifwambalifunkhakunja.
2Ndiposaganiziram’mitimamwaokutiinendikumbukira zoipazawozonse;zilipamasopanga
3Amakondweretsamfumundizoipazao,ndiakalongandi mabodzaao
4Onsendiachigololo,mongang’anjoyotenthedwandi wophikamkate,amenewalekakuwotcha,ataukanda mtanda,kufikirawatupitsa
5Tsikulamfumuyathuakalongaadwalitsandimabotoloa vinyo;anatambasuladzanjalakepamodzindionyoza
6Pakutianakonzekeretsamitimayaongating’anjo, pameneakulalira;m’maŵaitenthangatilawilamoto.
7Onseatenthangating’anjo,nadyaoweruzaao;mafumu aoonseagwa;palibemmodziwaiwoameneaitanakwa Ine.
8Efraimuwadzisanganizapakatipaanthu;Efraimundi kekewosatembenuzidwa
9Alendoadyamphamvuyace,ndipoiyesadziwa;inde imviziripaiye,komaiyesadziwa
10KunyadakwaIsrayelikumchitiraumbonipamasopake, ndipoiwosanabwererekwaYehovaMulunguwawo, kapenakumfunafunachifukwachazonsezi
11Efraimualingatinjiwayopusayopandamtima; 12Pameneapita,ndidzawayaliraukondewanga; ndidzawatsitsangatimbalamezam’mlengalenga;+ Ndidzawalanga+mongammenempingowawounamvera 13Tsokakwaiwo!pakutiandithawa;chionongekochawo! popezaanandilakwira;ngakhalendinawaombola,koma andinenerazonama
14Ndiposanandiitanendimtimawao,poliramaliropa mabediao;
15Ngakhalendawamangandikulimbitsamanjaawo, komaakundikonzerachoipa.
16Iwoabwerera,komaosatikwaWam'mwambamwamba; alingatiutawonyenga:akalongaaoadzagwandilupanga chifukwachaukaliwalilimelawo;
MUTU8
1Ikalipengapakamwapako+Iyeadzabwerangati chiwombankhangakumenyanandinyumbayaYehova,+ chifukwaanalakwirapanganolanga+ndikuphwanya malamuloanga
2Israyeliadzafuulirakwaine,Mulunguwanga,ife tikudziwaniInu
3Israyeliwatayacokoma;mdaniadzamtsata
4Anadziikiramafumu,komaosatimwaIne;anadzipangira akalonga,komainesindinalikudziŵa; 5Mwanawang’ombewakowakutaya,iweSamariya; mkwiyowangawawayakira;mpakalitiiwoasanakhale opandamlandu?
6PakutinalonsolinachokerakwaIsrayeli:mmisiri analipanga;chifukwachakesiMulungu;komamwanawa ng'ombewaSamariyaadzaphwanyidwa
7Pakutianafesamphepo,nadzatutakabvumvulu,alibe phesi;
8Israyeliwamezedwa:tsopanoadzakhalapakatipa amitundungatichotengerachosakondweretsa
9PakutiakwerakunkakuAsuri,ngatibuluwakuthengopa yekha;
10Inde,ngakhaleaganyumwaamitundu, ndidzawasonkhanitsatsopano,ndipoadzalirapang’ono chifukwachakatunduwamfumuyaakalonga.
11PopezaEfuraimuwachulukitsamaguwaansembekuti azichimwa,maguwaansembeadzachimwitsa
12Ndinamulemberazinthuzazikuluzam’chilamulo changa,komaanaziyesachinthuchachilendo
13Apheranyamayansembezanga,naidya;komaYehova sawalandira;tsopanoadzakumbukiramphulupuluzao, nadzalangazocimwazao;
14PakutiIsrayeliwaiwalaMlengiwake,namangaakachisi; ndipoYudawacurukitsamidziyamalinga;
MUTU9
1Usakondwera,Israyeli,ndicimwemwe,mongamitundu inayaanthu;pakutiwacitacigololokwaMulunguwako; 2Pansanjandimoponderamphesasizidzawadyetsa,ndipo vinyowatsopanoadzatheratu
3Sadzakhalam’dzikolaYehova;+KomaEfuraimu adzabwererakuIguputo+ndipoadzadyazodetsedwa m’Asuri
4SadzaperekansembezavinyokwaYehova,ndipo sizidzamkomera;onseakudyakoadzadetsedwa;pakuti mkatewamoyowaosudzalowam'nyumbayaYehova
5Mudzachitachiyanipatsikuloikika,nditsikula madyereroaYehova?
6Pakuti,tawonani,achokachifukwachachiwonongeko: Aiguptoadzawasonkhanitsa,Memfisiadzawaikam'manda; lunguzilidzawatengamalookondweretsaasiliva;minga idzakhalam'mahemamwao
7Masikuakulangaafika,masikuakubwezeraafika; Israyeliadzadziwa:Mnenerindiwopusa,munthuwauzimu ndiwamisala,chifukwachakuchulukakwamphulupulu yako,ndiudaniwaukulu.
8MlondawaEfraimuanalindiMulunguwanga;koma mnenerindiyemsamphawamsodzim’njirazakezonse, ndiudanim’nyumbayaMulunguwake.
9Iwoadziipitsakwambiri,mongam’masikuaGibeya; 10NdinapezaIsrayelingatimphesam’chipululu;Ndinaona makoloanungatizoyambakuchazamkuyunthawiyake yoyamba;ndizonyansazaozinalimongaanakonda
11KomaEfraimu,ulemererowaoudzaulukangati mbalame,osabala,osabala,osatengapakati.
12Ngakhalealeraanaao,ndidzawalandaanaao,kuti sadzatsalamunthu;
+13Efuraimu+mongandinaoneraTuro+wobzalidwa pamaloabwino,+komaEfuraimuadzatulutsaanaakekwa wophamnzake
14Apatseni,Yehova:Mudzapatsaciani?apatsenimimba yopitapaderandimabereouma
+15ZoipazawozonsezilikuGiligala+chifukwa kumenekondinawada,+chifukwachakuipakwazochita zawo+ndipondidzawathamangitsam’nyumbayanga, ndiposindidzawakondanso.
16Efraimuanakanthidwa,muzuwaowauma,sadzabala zipatso;
17Mulunguwangaadzawataya,chifukwasanamveraiye: ndipoadzakhalaoyendayendamwaamitundu
1Israyelindiyempesawopandakanthu,adzibalirayekha zipatso;mongamwaubwinowadzikolaceiwoanapanga mafanookoma.
2Mtimawawowagawanika;adzapasulamaguwaaoa nsembe,adzaonongamafanoao
3Pakutitsopanoadzati,Tilibemfumu,popezasitinaopa Yehova;tsonomfumuidzatichitirachiyani?
4Alankhulamau,kulumbiramonama,popanganapangano; 5AnthuokhalakuSamariyaadzachitamanthachifukwa chaanaang’ombeakuBetaveni,+pakutianthuake adzalilira,+ndiansembeakeameneanasangalalanawo chifukwachaulemererowake,+chifukwawachokapo
+6LidzaperekedwansokuAsuri+ngatimphatsokwa mfumuYarebe:+Efuraimuadzachitamanyazi+ndipo Isiraeliadzachitamanyazindiuphunguwake
7KomaSamariyamfumuyakeyadulidwangatithovu pamadzi.
+8MalookwezekaaAveni+omwenditchimolaIsiraeli adzawonongedwandipoadzatikwamapiri,Tiphimbeni; ndikwazitunda,Igwanipaife.
9Israyeli,wacimwakuyambiramasikuaGibeya, pamenepoanaima;
10Inendikufunakutindiwalanga;ndipoanthu adzawasonkhanira,pameneadzadzimangiriram’mizere yawoiwiri
11Efraimualingating’ombeyaikaziyophunzitsidwa bwino,yokondakupunthatirigu;komandinaolokapakhosi lakelokongola,ndidzamkweraEfraimu;Yudaadzalima, ndipoYakoboadzathyolazibumazake.
12Dzibzalireninokham’chilungamo,kololanichifundo; Limanimathithianu,pakutiyafikanthawiyofunafuna Yehova,kufikiraIyeatadza,nabvumbitsirainuchilungamo. 13Mwalimazoipa,mwakololamphulupulu;mwadya zipatsozamabodza:popezamunakhulupiriranjirayanu, ndiunyinjiwaamphamvuanu.
14Cifukwacacepadzaukaphokosopakatipaanthuako, ndimipandayakoyonseidzapasulidwa,mongamomwe SalimanianafunkhiraBetaribelitsikulankhondo;amayi anaphwanyidwapamodzindianaake
15Beteliadzakuchitiranimoterochifukwachazoipazanu zazikulu;
MUTU11
1PameneIsrayelianalimwana,ndinamkonda,ndipo ndinaitanamwanawangaacokekuAigupto.
2Pameneanawaitana,momwemonsoanawasiya;anaphera nsembeAbaala,nafukizirazifanizirozosema
3NdinaphunzitsansoEfraimukumuka,ndikuwagwira m’manja;komasanadziwakutindinawaciritsa.
4Ndinawakokandizingwezamunthu,ndizomangiraza chikondi;
5SadzabwererakudzikolaAigupto,komaAsuri adzakhalamfumuyake,chifukwaanakanakubwerera
6Ndipolupangalidzakhalapamidziyake,nidzanyeketsa nthambizake,ndikuidyachifukwachauphunguwao
7Ndipoanthuangaakundibwereram’mbuyo;
8Ndidzakuperekabwanji,iweEfraimu? ndidzakupulumutsabwanji,Israyeli?ndidzakusandutsa bwanjingatiAdima?ndidzakuyesabwanjingatiZeboimu?
mtimawangawatembenukamwaine,zolapazangazayaka pamodzi.
9Sindidzachitaukaliwamkwiyowanga,sindidzabwerera kuwonongaEfraimu;Woyerayopakatipanu:ndipo sindidzalowam’mudzi.
10AdzatsataYehova:adzabangulangatimkango; +11AdzanjenjemerangatimbalamekuchokerakuIguputo, +ngatinkhunda+kuchokeram’dzikolaAsuri,+ndipo ndidzawaikam’nyumbazawo,”+wateroYehova
12Efraimuwandizingandimabodza,ndinyumbaya Israyelindicinyengo;
MUTU12
1Efraimuadyamphepo,natsatamphepoyakum'mawa;+ IwoachitapanganondiAsuri,+ndipomafutaakupita nawokuIguputo
2YehovaalinsondimlandundiYuda,ndipoadzalanga Yakobomongamwanjirazace;adzambwezeramonga mwamachitidweace
3Iyeanatengam’balewakendichidendenem’mimba mwake,+ndipondimphamvuzake+anakhalandi mphamvundiMulungu
4Inde,analindimphamvupamngeloyo,napambana, nalira,nampemphaiye;
5Yehova,Mulunguwamakamu;Yehovandiye chikumbutsochake
6CifukwacacebwererakwaMulunguwako:sunga cifundondiciweruzo,nulindirireMulunguwako kosalekeza
7Iyendiwamalonda,miyesoyachinyengoilim’dzanja lake:akondakupondereza
8Efraimuanati,Komandalemera,ndapezachumachanga; 9NdipoinendineYehovaMulunguwakokuyambira m’dzikolaAigupto,ndidzakukhalitsaninsom’misasa, mongam’masikuamadyererooikidwiratu
+10Inendalankhulansokudzeramwaaneneri,+ndipo ndachulukitsamasomphenya+ndipondachitamafanizo kudzeramwaaneneri
11Kodim’Giliyadimulicholakwa?ndithu,iwondichabe; apherang'ombezamphongokuGiligala;indemaguwaa nsembeawoalingatimiundayam’mizereyaminda
12NdipoYakoboanathawirakudzikolaSuriya,ndipo Israyelianatumikirakutiapezemkazi,nawetankhosakuti apezemkazi
13NdipomwamneneriYehovaanatulutsaIsrayeli m’Aigupto,napulumutsidwandimneneri
14Efraimuanautsamkwiyowakekoopsa;
MUTU13
1PameneananenaEfraimukunjenjemera,anadzikuza m'Israyeli;komapameneanalakwiraBaala,iyeanafa 2Ndipotsopanoiwoakuchulukirakuchimwa, nadzipangiramafanooyengandisilivawawo,ndimafano mongamwalunthalawo,zonsezontchitozaamisiri; 3Chifukwachakeadzakhalangatimtambowam’mamawa, +ngatimameameneakuchokam’mamawa,+ngati mankhusuameneamaulutsidwandikamvuluvulupadwale, +ndiponsongatiutsiwochokeram’chochocho.
4KomainendineYehovaMulunguwakokuyambiraku dzikolaAigupto,sudzadziwamulunguwinakomaIne, pakutipalibempulumutsikomaIne
5Ndinakudziwanim’chipululu,m’dzikolachilala chachikulu.
6Mongamwamsipuwao,momwemoanakhuta;anakhuta, ndipomtimawaounakwezeka;chifukwachakeandiiwala Ine.
7Cifukwacacendidzakhalakwaiwongatimkango, Ndidzawayang’anirangatinyalugwe;
+8Ndidzakumananawongatichimbalangondo cholandidwaanaake,+ndipondidzang’ambachokopacha mtimawawo,+ndipopamenepondidzawadyangati mkango,+chilombochidzawakhadzula
9IweIsrayeli,wadziwonongawekha;komamwainemuli thandizolanu.
10Inendidzakhalamfumuyako;alikutiwina wakupulumutsam'midziyakoyonse?ndioweruzaako ameneunati,Ndipatsenimfumundiakalonga?
11Ndinakupatsamfumumumkwiyowanga,ndipo ndinamuchotsamuukaliwanga
12MphulupuluzaEfraimuzamangidwa;tchimolake labisika
13Zowawazamkaziwobalazidzamgwera:iyendimwana wopandanzeru;pakutisayenerakukhalitsam’maloobala ana 14Ndidzawaombolakumphamvuyakumanda; Ndidzawaombolakuimfa:Oimfa,ndidzakhalamiliriyako; Omanda,ndidzakhalachiwonongekochako:kulapa kudzabisidwapamasopanga
15Ngakhaleabalazipatsomwaabaleake,mphepoya kum’maŵaidzafika,mphepoyaYehovaidzakwera kuchokerakuchipululu,ndikasupewakeadzauma,ndi kasupewakeadzaphwa;adzafunkhachumacha zokondweretsazonse
16Samariyaadzakhalabwinja;pakutiwapandukira Mulunguwace;adzagwandilupanga;makandaao adzaphwanyidwa,ndiakaziaoapakatiadzatumbulidwa
MUTU14
1Israyeli,bwererakwaYehovaMulunguwako;pakuti wagwandimphulupuluyako.
2Tenganimau,nimutembenukirekwaYehova:Nenani kwaiye,Chotsanimphulupuluzonse,ndipomutilandireife okoma;
3Asurisadzatipulumutsa;sitidzakwerapaakavalo, sitidzanenansokwantchitoyamanjaathu,Inundinu milunguyathu;
4Ndidzachiritsakubwererakwawo,ndidzawakonda mwaufulu:pakutimkwiyowangawamcokera
5NdidzakhalakwaIsrayelingatimame; 6Nthambizakezidzaphuka,ndikukongolakwake kudzakhalangatimtengowaazitona,ndifungolakengati Lebano
7Iwookhalamumthunziwakeadzabwerera;iwo adzakhalandimoyongatitirigu,nadzaphukangatimpesa; kununkhirakwakekudzakhalangativinyowakuLebano
8Efraimuadzati,Ndilindichiyaninsondimafano? Ndinamumva,ndipondinamusunga:ndilingatimtengo wamlombwawauwisiKwainendizipatsozako
9Ndanialiwanzeru,nadzazindikiraizi?wanzeru, nadzawazindikira?pakutinjirazaYehovazilizoongoka, ndipoolungamaadzayendamo;komaolakwaadzagwamo